Rute 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma iye powayankha anali kunena kuti: “Musanditchulenso kuti Naomi,* muzinditchula kuti Mara,* chifukwa Wamphamvuyonse+ wachititsa moyo wanga kukhala wowawa kwambiri.+ 1 Samueli 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho Samueli anamuuza mawu onse ndipo sanam’bisire kanthu. Pamenepo Eli anati: “Ndi Yehova amene wanena. Achite zimene akuona kuti n’zabwino.”+ Yobu 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndichitireni chifundo anzanganu, ndichitireni chifundo,+Chifukwa dzanja la Mulungu landikhudza.+
20 Koma iye powayankha anali kunena kuti: “Musanditchulenso kuti Naomi,* muzinditchula kuti Mara,* chifukwa Wamphamvuyonse+ wachititsa moyo wanga kukhala wowawa kwambiri.+
18 Choncho Samueli anamuuza mawu onse ndipo sanam’bisire kanthu. Pamenepo Eli anati: “Ndi Yehova amene wanena. Achite zimene akuona kuti n’zabwino.”+