Rute 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 kodi mungawadikirirebe mpaka atakula? Kodi mungadzisungebe osakwatiwa powadikirira? Ayi ndithu ana anga, zimene zinakuchitikirani zimandiwawa kwambiri, pakuti dzanja la Yehova landiukira.”+ 1 Samueli 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho Samueli anamuuza mawu onse ndipo sanam’bisire kanthu. Pamenepo Eli anati: “Ndi Yehova amene wanena. Achite zimene akuona kuti n’zabwino.”+ Yobu 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndichitireni chifundo anzanganu, ndichitireni chifundo,+Chifukwa dzanja la Mulungu landikhudza.+ Yesaya 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 M’tsiku limenelo+ ndithu udzanena kuti: “Ndikukuthokozani inu Yehova pakuti ngakhale munandikwiyira, mkwiyo wanu unabwerera pang’onopang’ono+ ndipo munanditonthoza.+
13 kodi mungawadikirirebe mpaka atakula? Kodi mungadzisungebe osakwatiwa powadikirira? Ayi ndithu ana anga, zimene zinakuchitikirani zimandiwawa kwambiri, pakuti dzanja la Yehova landiukira.”+
18 Choncho Samueli anamuuza mawu onse ndipo sanam’bisire kanthu. Pamenepo Eli anati: “Ndi Yehova amene wanena. Achite zimene akuona kuti n’zabwino.”+
12 M’tsiku limenelo+ ndithu udzanena kuti: “Ndikukuthokozani inu Yehova pakuti ngakhale munandikwiyira, mkwiyo wanu unabwerera pang’onopang’ono+ ndipo munanditonthoza.+