Rute 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munthuyo dzina lake anali Elimeleki, ndipo mkazi wake anali Naomi. Mayina a ana akewo anali Maloni ndi Kiliyoni. Anthuwa anali a ku Betelehemu Efurata+ wa ku Yuda. Ndipo anafika m’dziko la Mowabu ndi kukhazikika kumeneko.
2 Munthuyo dzina lake anali Elimeleki, ndipo mkazi wake anali Naomi. Mayina a ana akewo anali Maloni ndi Kiliyoni. Anthuwa anali a ku Betelehemu Efurata+ wa ku Yuda. Ndipo anafika m’dziko la Mowabu ndi kukhazikika kumeneko.