-
Yobu 10:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Mudzabweretsa mboni zanu zatsopano pamaso panga,
Ndipo mudzakulitsa mkwiyo wanu pa ine.
Mavuto anga akungotsatizanatsatizana.
-