Rute 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Panali munthu wina wolemera kwambiri+ yemwe anali wachibale+ wa mwamuna wake wa Naomi. Dzina lake anali Boazi,+ wa kubanja la Elimeleki. Rute 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Salimoni+ anabereka Boazi, Boazi+ anabereka Obedi, 1 Mbiri 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Naasoni anabereka Salima,+ Salima anabereka Boazi,+
2 Panali munthu wina wolemera kwambiri+ yemwe anali wachibale+ wa mwamuna wake wa Naomi. Dzina lake anali Boazi,+ wa kubanja la Elimeleki.