-
Salimo 104:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Amameretsa msipu kuti nyama zidye,+
Ndipo amameretsa mbewu kuti anthu agwiritse ntchito.+
Amachita zimenezi kuti chakudya chituluke m’nthaka,+
-