Yobu 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kodi okalamba si paja amakhala ndi nzeru,+Ndipo amene akhala masiku ambiri si paja amamvetsa zinthu? Miyambo 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Njira ya munthu wopusa imakhala yolondola m’maso mwake,+ koma womvera malangizo ndi wanzeru.+ 1 Akorinto 15:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Musasocheretsedwe. Kugwirizana ndi anthu oipa kumawononga makhalidwe abwino.+ Tito 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chimodzimodzinso akazi achikulire.+ Akhale ndi khalidwe loyenera anthu opembedza. Asakhale amiseche,+ kapena akapolo a vinyo wambiri, koma akhale aphunzitsi a zinthu zabwino,
12 Kodi okalamba si paja amakhala ndi nzeru,+Ndipo amene akhala masiku ambiri si paja amamvetsa zinthu?
3 Chimodzimodzinso akazi achikulire.+ Akhale ndi khalidwe loyenera anthu opembedza. Asakhale amiseche,+ kapena akapolo a vinyo wambiri, koma akhale aphunzitsi a zinthu zabwino,