Deuteronomo 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma nonsenu amene mukumamatira+ kwa Yehova Mulungu wanu muli ndi moyo lero. Deuteronomo 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Muziopa Yehova Mulungu wanu.+ Muzim’tumikira,+ kum’mamatira+ ndi kulumbira pa dzina lake.+ Rute 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova akudalitse chifukwa cha zimene wachita,+ ndipo Yehova, Mulungu wa Isiraeli akufupe mokwanira.+ Iye amene m’mapiko mwake wathawiramo ndi kupezamo chitetezo.”+ 1 Mafumu 8:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 “Komanso mlendo+ amene sali mmodzi wa anthu anu Aisiraeli, amene wabwera kuchokera kudziko lakutali chifukwa cha dzina lanu+
12 Yehova akudalitse chifukwa cha zimene wachita,+ ndipo Yehova, Mulungu wa Isiraeli akufupe mokwanira.+ Iye amene m’mapiko mwake wathawiramo ndi kupezamo chitetezo.”+
41 “Komanso mlendo+ amene sali mmodzi wa anthu anu Aisiraeli, amene wabwera kuchokera kudziko lakutali chifukwa cha dzina lanu+