Rute 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako, anawo anakwatira akazi achimowabu.+ Wina dzina lake anali Olipa, wina anali Rute.+ Ndipo anakhalabe kumeneko zaka pafupifupi 10. 2 Mafumu 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zaka 7 zija zitatha, mayiyo anabwerera kuchokera kudziko la Afilisiti n’kupita kukadandaulira mfumu+ kuti imupatse nyumba yake ndi munda wake.
4 Kenako, anawo anakwatira akazi achimowabu.+ Wina dzina lake anali Olipa, wina anali Rute.+ Ndipo anakhalabe kumeneko zaka pafupifupi 10.
3 Zaka 7 zija zitatha, mayiyo anabwerera kuchokera kudziko la Afilisiti n’kupita kukadandaulira mfumu+ kuti imupatse nyumba yake ndi munda wake.