Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 1:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Kenako anadzuka m’mawa kwambiri n’kugwada ndi kuwerama mpaka nkhope zawo pansi pamaso pa Yehova. Atatero anabwerera kunyumba kwawo ku Rama.+ Ndiyeno Elikana anagona+ ndi mkazi wake Hana, ndipo Yehova anayamba kum’kumbukira.+

  • 1 Samueli 7:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Akazungulirazungulira, anali kubwerera ku Rama,+ chifukwa kumeneko n’kumene kunali nyumba yake, ndipo anali kuweruza Isiraeli ali kumeneko. Komanso iye anamangira Yehova guwa lansembe kumeneko.+

  • 1 Samueli 28:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Tsopano Samueli anali atamwalira ndipo Aisiraeli anali atamulira ndi kumuika m’manda mumzinda wakwawo ku Rama.+ Ndipo Sauli anali atachotsa anthu olankhula ndi mizimu ndi akatswiri olosera zam’tsogolo m’dzikolo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena