1 Samueli 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako anadzuka mʼmawa ndipo atalambira Yehova anabwerera kunyumba kwawo ku Rama.+ Ndiyeno Elikana anagona ndi mkazi wake Hana ndipo Yehova anamukumbukira.+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:19 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 16
19 Kenako anadzuka mʼmawa ndipo atalambira Yehova anabwerera kunyumba kwawo ku Rama.+ Ndiyeno Elikana anagona ndi mkazi wake Hana ndipo Yehova anamukumbukira.+