1 Samueli 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma Yonatani, mwana wa Sauli, anali kukonda kwambiri Davide.+ Choncho Yonatani anauza Davide kuti: “Sauli, bambo anga, akufuna kukupha. Chonde, mawa m’mawa ukhale wosamala. Ukakhale pamalo obisika ndipo ukabisalebe choncho.+ 1 Samueli 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Poyankha, Davide anauza Yonatani kuti: “Mawatu ndi tsiku lokhala mwezi,+ ndipo mosalephera ndiyenera kukadya pamodzi ndi mfumu. Ndiyeno iweyo undilole ndipite kuti ndikabisale+ kutchire mpaka mkuja madzulo.
2 Koma Yonatani, mwana wa Sauli, anali kukonda kwambiri Davide.+ Choncho Yonatani anauza Davide kuti: “Sauli, bambo anga, akufuna kukupha. Chonde, mawa m’mawa ukhale wosamala. Ukakhale pamalo obisika ndipo ukabisalebe choncho.+
5 Poyankha, Davide anauza Yonatani kuti: “Mawatu ndi tsiku lokhala mwezi,+ ndipo mosalephera ndiyenera kukadya pamodzi ndi mfumu. Ndiyeno iweyo undilole ndipite kuti ndikabisale+ kutchire mpaka mkuja madzulo.