1 Samueli 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Poyankha, Davide anauza Yonatani kuti: “Mawatu ndi tsiku lokhala mwezi,+ ndipo mosalephera ndiyenera kukadya pamodzi ndi mfumu. Ndiyeno iweyo undilole ndipite kuti ndikabisale+ kutchire mpaka mkuja madzulo.
5 Poyankha, Davide anauza Yonatani kuti: “Mawatu ndi tsiku lokhala mwezi,+ ndipo mosalephera ndiyenera kukadya pamodzi ndi mfumu. Ndiyeno iweyo undilole ndipite kuti ndikabisale+ kutchire mpaka mkuja madzulo.