Levitiko 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “‘Mkazi akagonana ndi mwamuna, onse awiri azisamba thupi lonse, ndipo azikhala odetsedwa+ kufikira madzulo. Deuteronomo 23:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakati panu pakakhala mwamuna amene sali woyera chifukwa cha chodetsa chochitika usiku,+ azipita kunja kwa msasa. Asalowe mumsasamo.+
18 “‘Mkazi akagonana ndi mwamuna, onse awiri azisamba thupi lonse, ndipo azikhala odetsedwa+ kufikira madzulo.
10 Pakati panu pakakhala mwamuna amene sali woyera chifukwa cha chodetsa chochitika usiku,+ azipita kunja kwa msasa. Asalowe mumsasamo.+