Salimo 31:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Simunandipereke m’manja mwa adani.+Mwapondetsa phazi langa pamalo otakasuka.+ Salimo 62:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye ndiye thanthwe langa ndi chipulumutso changa, malo anga okwezeka ndiponso achitetezo.+Sindidzagwedezeka kwambiri.+ Salimo 94:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova amadziwa kuti maganizo a anthu ali ngati mpweya wotuluka m’mphuno.+ Salimo 118:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kuthawira kwa Yehova n’kwabwino+Kusiyana ndi kudalira munthu wochokera kufumbi.+
2 Iye ndiye thanthwe langa ndi chipulumutso changa, malo anga okwezeka ndiponso achitetezo.+Sindidzagwedezeka kwambiri.+