1 Samueli 18:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Apanso Sauli anachita mantha kwambiri ndi Davide, moti anali kudana ndi Davide nthawi zonse.+ 1 Samueli 20:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Atatero, Sauli anaponya mkondo wake kuti amulase.+ Pamenepo Yonatani anadziwa kuti bambo ake anatsimikiza mtima kupha Davide.+ Salimo 112:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Woipa adzaona zimenezi ndipo adzasautsika.+ ש [Shin]Adzakukuta mano ndi kusungunuka.+ ת [Taw]Chikhumbo cha anthu oipa chidzatha.+ Miyambo 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Zolakalaka za anthu olungama, ndithu n’zabwino.+ Chiyembekezo cha oipa chimabweretsa mkwiyo woopsa.+
33 Atatero, Sauli anaponya mkondo wake kuti amulase.+ Pamenepo Yonatani anadziwa kuti bambo ake anatsimikiza mtima kupha Davide.+
10 Woipa adzaona zimenezi ndipo adzasautsika.+ ש [Shin]Adzakukuta mano ndi kusungunuka.+ ת [Taw]Chikhumbo cha anthu oipa chidzatha.+
23 Zolakalaka za anthu olungama, ndithu n’zabwino.+ Chiyembekezo cha oipa chimabweretsa mkwiyo woopsa.+