1 Samueli 26:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kwa ine, n’zosatheka!+ Sindingachite zimenezi pamaso pa Yehova.+ Sindingatambasule dzanja langa+ ndi kukantha wodzozedwa wa Yehova.+ Choncho, tiye titenge mkondo umene uli chakumutu kwakewo, ndi mtsuko wa madziwo tizipita.” 1 Mafumu 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Atayang’ana, anaona kuti kumutu kwake kuli chikho cha madzi ndi mkate wozungulira+ uli pamiyala yotentha. Ndipo Eliya anayamba kudya ndi kumwa, kenako anagonanso.
11 Kwa ine, n’zosatheka!+ Sindingachite zimenezi pamaso pa Yehova.+ Sindingatambasule dzanja langa+ ndi kukantha wodzozedwa wa Yehova.+ Choncho, tiye titenge mkondo umene uli chakumutu kwakewo, ndi mtsuko wa madziwo tizipita.”
6 Atayang’ana, anaona kuti kumutu kwake kuli chikho cha madzi ndi mkate wozungulira+ uli pamiyala yotentha. Ndipo Eliya anayamba kudya ndi kumwa, kenako anagonanso.