-
1 Samueli 4:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Ndiyeno mwamunayo atangotchula za likasa la Mulungu woona, Eli anagwa chagada kuchoka pampando, ali pachipatapo. Chotero khosi lake linathyoka ndipo anafa, pakuti anali wokalamba ndi wonenepa kwambiri. Eli anali ataweruza Isiraeli zaka 40.
-