Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 36:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Elifazi mwana wa Esau anali ndi mdzakazi dzina lake Timina.+ Patapita nthawi, mdzakaziyu anaberekera Elifazi mwana wamwamuna dzina lake Amaleki.+ Amenewa ndiwo anali ana a Ada mkazi wa Esau.

  • Ekisodo 17:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Tsopano Yehova anauza Mose kuti: “Lemba zimenezi m’buku monga chikumbutso+ ndi kumuuza Yoswa kuti, ‘M’kupita kwa nthawi ndidzafafaniziratu Aamaleki padziko lapansi* ndipo sadzakumbukika n’komwe.’”+

  • 1 Samueli 15:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Yehova wa makamu+ wanena kuti, ‘Ndibwezera+ Aamaleki chifukwa choukira Aisiraeli panjira, pamene Aisiraeliwo anali kutuluka mu Iguputo.+

  • 1 Samueli 27:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndiyeno Davide pamodzi ndi amuna amene anali kuyenda naye anapita kukathira nkhondo Agesuri,+ Agirezi ndi Aamaleki.+ Mitundu imeneyi inali kukhala m’dera loyambira ku Telami+ kukafika ku Shura,+ mpaka kukafika kudziko la Iguputo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena