Numeri 27:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ngati bambo ake analibe azichimwene awo, muzipereka cholowa chake kwa wachibale wake wapafupi wa ku banja lawo,+ ndipo azitenga cholowacho kukhala chake. Ili likhale lamulo kwa ana a Isiraeli mwa chigamulo changa, monga Yehova walamulira Mose.’”
11 Ngati bambo ake analibe azichimwene awo, muzipereka cholowa chake kwa wachibale wake wapafupi wa ku banja lawo,+ ndipo azitenga cholowacho kukhala chake. Ili likhale lamulo kwa ana a Isiraeli mwa chigamulo changa, monga Yehova walamulira Mose.’”