1 Samueli 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo Hana anaimirira atadya ndi kumwa ku Silo. Apa n’kuti Eli wansembe atakhala pampando, pakhomo la kachisi+ wa Yehova. 1 Samueli 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Samueli anagonabe mpaka m’mawa. Atadzuka anatsegula zitseko za nyumba ya Yehova,+ koma anaopa kuuza Eli za masomphenya amene anaona.+ Salimo 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma ine ndidzalowa m’nyumba yanu+Chifukwa cha kuchuluka kwa kukoma mtima kwanu kosatha.+Ndidzawerama nditayang’ana kumene kuli kachisi wanu wopatulika chifukwa chokuopani.+
9 Pamenepo Hana anaimirira atadya ndi kumwa ku Silo. Apa n’kuti Eli wansembe atakhala pampando, pakhomo la kachisi+ wa Yehova.
15 Ndiyeno Samueli anagonabe mpaka m’mawa. Atadzuka anatsegula zitseko za nyumba ya Yehova,+ koma anaopa kuuza Eli za masomphenya amene anaona.+
7 Koma ine ndidzalowa m’nyumba yanu+Chifukwa cha kuchuluka kwa kukoma mtima kwanu kosatha.+Ndidzawerama nditayang’ana kumene kuli kachisi wanu wopatulika chifukwa chokuopani.+