Yoweli 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Sonkhanitsani anthu onse pamodzi ndipo muyeretse mpingo.+ Sonkhanitsani amuna achikulire. Sonkhanitsani pamodzi ana ndi makanda oyamwa.+ Mkwati atuluke m’chipinda chake ndipo mkwatibwi atuluke kumalo ake ogona.
16 Sonkhanitsani anthu onse pamodzi ndipo muyeretse mpingo.+ Sonkhanitsani amuna achikulire. Sonkhanitsani pamodzi ana ndi makanda oyamwa.+ Mkwati atuluke m’chipinda chake ndipo mkwatibwi atuluke kumalo ake ogona.