Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 17:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Mwasanthula mtima wanga, mwandifufuza usiku,+

      Ndipo mwandiyenga. Mudzaona kuti sindinaganizire kuchita choipa chilichonse.+

      Pakamwa panga sipadzaphwanya malamulo.+

  • Salimo 37:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Ona munthu wosalakwa ndipo yang’anitsitsa munthu wolungama,+

      Pakuti tsogolo la munthu ameneyu ndi lamtendere.+

  • Yohane 18:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Pilato anafunsa kuti: “Choonadi n’chiyani?”

      Atangofunsa funso limeneli, anatuluka ndi kupitanso kumene kunali Ayuda kuja, ndi kuwauza kuti: “Ineyo sindikupeza cholakwa chilichonse mwa munthu ameneyu.+

  • Machitidwe 20:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Sindinasirire mwa nsanje siliva, golide kapena chovala cha munthu.+

  • 1 Atesalonika 2:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndipotu, sitinayambe talankhulapo mawu okuyamikirani mwachinyengo,+ (monga mukudziwira), kapena kuchita zachiphamaso+ chifukwa cha kusirira kwa nsanje.+ Mulungu ndiye mboni yathu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena