Miyambo 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Khulupirira Yehova ndi mtima wako wonse,+ ndipo usadalire luso lako lomvetsa zinthu.+ Miyambo 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pali njira yooneka ngati yowongoka kwa munthu,+ koma mapeto ake ndi imfa.+ Miyambo 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mumtima mwa munthu mumakhala zolinga zambiri,+ koma zolinga za Yehova n’zimene zidzakwaniritsidwe.+
21 Mumtima mwa munthu mumakhala zolinga zambiri,+ koma zolinga za Yehova n’zimene zidzakwaniritsidwe.+