Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 7:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Amuna 300+ aja anapitiriza kuliza malipenga,+ ndipo Yehova anachititsa Amidiyani kuukirana okhaokha mumsasa wonsewo.+ Anthu onse a mumsasawo anathawa mpaka kukafika ku Beti-sita, ndi ku Zerera mpaka kumalire kwa mzinda wa Abele-mehola+ pafupi ndi Tabati.

  • 1 Samueli 14:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Choncho Sauli ndi anthu onse amene anali naye anasonkhana pamodzi kuti apite kukamenyana ndi Afilisiti.+ Ndiyeno anayenda mpaka kukafika kumene kunali nkhondoko, ndipo anapeza kuti aphana okhaokha ndi lupanga,+ moti chipwirikiti chake chinali chosaneneka.

  • 2 Mbiri 20:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ana a Amoni ndi ana a Mowabu anaukira anthu okhala kudera lamapiri la Seiri+ ndipo anawapha ndi kuwamaliza. Atatha kupha anthu a ku Seiri, iwo anaphana okhaokha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena