Yobu 36:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa mawu anga ndithu si onama.Wodziwa bwino zinthu kwambiri+ ali ndi inu. Yobu 37:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kodi mukudziwa mmene mtambo umaimira,+Ndiponso ntchito zodabwitsa za yemwe amadziwa zinthu bwino kwambiri?+ Salimo 147:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ambuye wathu ndi wamkulu ndipo ali ndi mphamvu zochuluka.+Nzeru zake zilibe malire.+ Aroma 11:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndithudi, madalitso amene Mulungu amapereka ndi ochuluka kwambiri.+ Nzeru+ zake n’zozama, ndiponso iye ndi wodziwa zinthu kwambiri.+ Ziweruzo zake ndi zosasanthulika,+ ndipo ndani angatulukire njira zake?
16 Kodi mukudziwa mmene mtambo umaimira,+Ndiponso ntchito zodabwitsa za yemwe amadziwa zinthu bwino kwambiri?+
33 Ndithudi, madalitso amene Mulungu amapereka ndi ochuluka kwambiri.+ Nzeru+ zake n’zozama, ndiponso iye ndi wodziwa zinthu kwambiri.+ Ziweruzo zake ndi zosasanthulika,+ ndipo ndani angatulukire njira zake?