Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Tsopano ana aamuna a Eli anali anthu opanda pake.+ Iwo anali kunyalanyaza Yehova.+

  • 1 Samueli 2:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ndiyeno Eli anali wokalamba kwambiri ndipo anamva+ zonse zimene ana ake anali kuchitira+ Aisiraeli onse, komanso anamva kuti anali kugona ndi akazi+ otumikira pakhomo la chihema chokumanako.+

  • 1 Samueli 2:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Ndipo chizindikiro chako chimene chidzachitikira ana ako awiri Hofeni ndi Pinihasi+ ndi ichi: Onse awiri adzafa tsiku limodzi.+

  • 1 Samueli 4:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Choncho munthu wobweretsa uthengayo anayankha kuti: “Aisiraeli athawa pamaso pa Afilisiti, ndipo agonjetsedwa koopsa.+ Ana anunso awiri, Hofeni ndi Pinihasi,+ aphedwa. Ngakhalenso likasa la Mulungu woona lalandidwa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena