Ekisodo 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Dzanja lanu lamanja, inu Yehova, likusonyeza kupambana kwa mphamvu zake.+Dzanja lanu lamanja, inu Yehova, limaphwanya mdani.+ Salimo 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Dzanja lanu lidzapeza adani anu onse.+Dzanja lanu lamanja lidzapeza odana nanu. Salimo 92:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti taonani adani anu, inu Yehova!+Adani anu onse adzatha!+Anthu onse ochita zopweteka anzawo adzamwazikana.+
6 Dzanja lanu lamanja, inu Yehova, likusonyeza kupambana kwa mphamvu zake.+Dzanja lanu lamanja, inu Yehova, limaphwanya mdani.+
9 Pakuti taonani adani anu, inu Yehova!+Adani anu onse adzatha!+Anthu onse ochita zopweteka anzawo adzamwazikana.+