Salimo 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo adzanena kuti: “Inetu ndakhazika mfumu yanga+Pa Ziyoni,+ phiri langa lopatulika.”+ Salimo 45:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Mtima wanga wagalamuka chifukwa cha nkhani yosangalatsa.+Ine ndikuti: “Nyimbo yangayi ikunena za mfumu.”+Lilime langa likhale ngati cholembera+ cha wokopera malemba waluso.+ Salimo 110:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 110 Yehova wauza Ambuye wanga kuti:+“Khala kudzanja langa lamanja+Kufikira nditaika adani ako monga chopondapo mapazi ako.”+ Yesaya 32:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Taonani! Mfumu+ idzalamulira mwachilungamo,+ ndipo akalonga+ adzalamuliranso mwachilungamo. Mateyu 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tsopano Yesu anayandikira ndi kulankhula nawo kuti: “Ulamuliro wonse+ waperekedwa kwa ine kumwamba ndi padziko lapansi.
45 Mtima wanga wagalamuka chifukwa cha nkhani yosangalatsa.+Ine ndikuti: “Nyimbo yangayi ikunena za mfumu.”+Lilime langa likhale ngati cholembera+ cha wokopera malemba waluso.+
110 Yehova wauza Ambuye wanga kuti:+“Khala kudzanja langa lamanja+Kufikira nditaika adani ako monga chopondapo mapazi ako.”+
18 Tsopano Yesu anayandikira ndi kulankhula nawo kuti: “Ulamuliro wonse+ waperekedwa kwa ine kumwamba ndi padziko lapansi.