2 Samueli 3:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ine lero ndafooka ngakhale kuti ndine mfumu yodzozedwa,+ ndipo ine ndikuona kuti amuna awa, ana a Zeruya,+ achita nkhanza kwambiri.+ Yehova abwezere aliyense wochita zinthu zoipa mogwirizana ndi kuipa kwake.”+ 2 Samueli 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma mfumu inati: “Ndili nanu chiyani+ inu ana a Zeruya?+ Musiyeni anyoze+ chifukwa Yehova wamuuza kuti,+ ‘Munyoze Davide!’ Choncho ndani angamufunse kuti, ‘N’chifukwa chiyani iwe wachita zimenezi?’”+
39 Ine lero ndafooka ngakhale kuti ndine mfumu yodzozedwa,+ ndipo ine ndikuona kuti amuna awa, ana a Zeruya,+ achita nkhanza kwambiri.+ Yehova abwezere aliyense wochita zinthu zoipa mogwirizana ndi kuipa kwake.”+
10 Koma mfumu inati: “Ndili nanu chiyani+ inu ana a Zeruya?+ Musiyeni anyoze+ chifukwa Yehova wamuuza kuti,+ ‘Munyoze Davide!’ Choncho ndani angamufunse kuti, ‘N’chifukwa chiyani iwe wachita zimenezi?’”+