Salimo 37:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Usapse mtima ndipo pewa kukwiya.+Usapse mtima kuti ungachite choipa.+ 1 Petulo 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamene anali kunenedwa zachipongwe,+ sanabwezere zachipongwe.+ Pamene anali kuvutika,+ sanawopseze, koma anali kudzipereka kwa iye+ amene amaweruza molungama.
23 Pamene anali kunenedwa zachipongwe,+ sanabwezere zachipongwe.+ Pamene anali kuvutika,+ sanawopseze, koma anali kudzipereka kwa iye+ amene amaweruza molungama.