Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 9:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Iweyo, ana ako aamuna ndi antchito ako, muzimulimira munda wake ndi kumukololera kuti anthu a m’nyumba ya mdzukulu wa mbuye wako azikhala ndi chakudya chimene azidya. Koma Mefiboseti, mdzukulu wa mbuye wako, azidya chakudya patebulo langa nthawi zonse.”+

      Tsopano Ziba anali ndi ana aamuna 15 ndi antchito 20.+

  • Miyambo 11:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Munthu wopatsa mowolowa manja adzalandira mphoto,+ ndipo wothirira ena mosaumira nayenso adzathiriridwa mosaumira.+

  • Mateyu 7:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Zinthu zonse zimene mukufuna kuti anthu akuchitireni,+ inunso muwachitire zomwezo, pakuti n’zimene Chilamulo ndi Zolemba za aneneri zimafuna.+

  • Luka 6:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Khalani opatsa ndipo inunso anthu adzakupatsani.+ Adzakhuthulira m’matumba anu muyezo wabwino, wotsendereka, wokhutchumuka ndi wosefukira. Pakuti muyezo umene mukuyezera ena, iwonso adzakuyezerani womwewo.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena