Mateyu 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 pakuti chiweruzo chimene mukuweruza nacho ena inunso mudzaweruzidwa nacho.+ Ndipo muyezo umene mukuyezera ena, iwonso adzakuyezerani womwewo.+ Maliko 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Anawauzanso kuti: “Samalani zimene mukumvazi.+ Muyezo umene mukuyezera, nanunso adzakuyezerani womwewo.+ Inde, adzakuwonjezerani zochuluka.+
2 pakuti chiweruzo chimene mukuweruza nacho ena inunso mudzaweruzidwa nacho.+ Ndipo muyezo umene mukuyezera ena, iwonso adzakuyezerani womwewo.+
24 Anawauzanso kuti: “Samalani zimene mukumvazi.+ Muyezo umene mukuyezera, nanunso adzakuyezerani womwewo.+ Inde, adzakuwonjezerani zochuluka.+