2 Samueli 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo anthu onse a Isiraeli anayamba kuchoka kwa Davide ndi kutsatira Sheba mwana wa Bikiri.+ Koma anthu a ku Yuda, kuyambira ku Yorodano mpaka ku Yerusalemu anamamatira mfumu yawo.+ 2 Samueli 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsopano mfumu inauza Amasa+ kuti: “Ndisonkhanitsire anthu a mu Yuda m’masiku atatu, ndipo iwe uime pano.”
2 Pamenepo anthu onse a Isiraeli anayamba kuchoka kwa Davide ndi kutsatira Sheba mwana wa Bikiri.+ Koma anthu a ku Yuda, kuyambira ku Yorodano mpaka ku Yerusalemu anamamatira mfumu yawo.+
4 Tsopano mfumu inauza Amasa+ kuti: “Ndisonkhanitsire anthu a mu Yuda m’masiku atatu, ndipo iwe uime pano.”