2 Samueli 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye anawapereka m’manja mwa Agibeoni, ndipo Agibeoniwo anaonetsa mitembo ya ana aamuna a Sauliwo kwa Yehova+ paphiri, moti onse 7 anafera limodzi. Iwo anaphedwa m’masiku oyambirira a nyengo yokolola, kuchiyambi kwa nyengo yokolola balere.+
9 Iye anawapereka m’manja mwa Agibeoni, ndipo Agibeoniwo anaonetsa mitembo ya ana aamuna a Sauliwo kwa Yehova+ paphiri, moti onse 7 anafera limodzi. Iwo anaphedwa m’masiku oyambirira a nyengo yokolola, kuchiyambi kwa nyengo yokolola balere.+