Yesaya 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Taonani! Mulungu ndiye chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+ pakuti Ya* Yehova ndiye mphamvu zanga+ ndi nyonga zanga,+ ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+ Luka 1:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Ndipo mzimu wanga sungaleke kusefukira+ ndi chimwemwe mwa Mulungu, Mpulumutsi wanga.+ Tito 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komatu Mpulumutsi+ wathu Mulungu, anaonetsa+ kukoma mtima+ ndi kukonda anthu.
2 Taonani! Mulungu ndiye chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+ pakuti Ya* Yehova ndiye mphamvu zanga+ ndi nyonga zanga,+ ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+