Deuteronomo 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Choncho anthu inu munayandikira ndi kuimirira m’munsi mwa phiri. Phiri limenelo linali kuyaka moto mpaka kumwamba, ndipo kunali mdima ndi mtambo wakuda.+ 1 Mafumu 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa nthawi imeneyo Solomo anati: “Yehova anati adzakhala mu mdima wandiweyani.+ Salimo 18:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye anaweramitsa kumwamba n’kutsika.+Mdima wandiweyani unali kunsi kwa mapazi ake. Salimo 97:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mitambo ndi mdima wandiweyani zamuzungulira.+Chilungamo ndi chiweruzo ndizo malo okhazikika a mpando wake wachifumu.+
11 “Choncho anthu inu munayandikira ndi kuimirira m’munsi mwa phiri. Phiri limenelo linali kuyaka moto mpaka kumwamba, ndipo kunali mdima ndi mtambo wakuda.+
2 Mitambo ndi mdima wandiweyani zamuzungulira.+Chilungamo ndi chiweruzo ndizo malo okhazikika a mpando wake wachifumu.+