Ekisodo 20:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho anthuwo anaimabe patali pomwepo, koma Mose anayandikira mtambo wakuda uja kumene kunali Mulungu woona.+ Deuteronomo 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Yehova analankhula Mawu* amenewa mokweza kumpingo wanu wonse, kuchokera pakati pa moto m’phiri,+ pamene kunachita mtambo wakuda ndi mdima wandiweyani, ndipo pa Mawuwo sanawonjezerepo kalikonse. Kenako anawalemba pamiyala iwiri yosema n’kundipatsa.+ Salimo 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako anapanga mdima kukhala malo ake obisalamo,+Panali madzi akuda ndi mtambo wakuda,Zimene zinamuzungulira ngati msasa wake.+ Salimo 97:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mitambo ndi mdima wandiweyani zamuzungulira.+Chilungamo ndi chiweruzo ndizo malo okhazikika a mpando wake wachifumu.+
21 Choncho anthuwo anaimabe patali pomwepo, koma Mose anayandikira mtambo wakuda uja kumene kunali Mulungu woona.+
22 “Yehova analankhula Mawu* amenewa mokweza kumpingo wanu wonse, kuchokera pakati pa moto m’phiri,+ pamene kunachita mtambo wakuda ndi mdima wandiweyani, ndipo pa Mawuwo sanawonjezerepo kalikonse. Kenako anawalemba pamiyala iwiri yosema n’kundipatsa.+
11 Kenako anapanga mdima kukhala malo ake obisalamo,+Panali madzi akuda ndi mtambo wakuda,Zimene zinamuzungulira ngati msasa wake.+
2 Mitambo ndi mdima wandiweyani zamuzungulira.+Chilungamo ndi chiweruzo ndizo malo okhazikika a mpando wake wachifumu.+