Salimo 18:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Anatambasula dzanja lake kuchokera kumwamba ndi kunditenga,+Anandivuula m’madzi akuya.+ Salimo 144:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tambasulani manja anu kuchokera kumwamba.+Ndimasuleni ndi kundilanditsa m’madzi ambiri.+Mundilanditse m’manja mwa anthu achilendo,+
7 Tambasulani manja anu kuchokera kumwamba.+Ndimasuleni ndi kundilanditsa m’madzi ambiri.+Mundilanditse m’manja mwa anthu achilendo,+