2 Samueli 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anatambasula dzanja lake kuchokera kumwamba ndi kunditenga,+Anandivuula m’madzi akuya.+ Salimo 18:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Anatambasula dzanja lake kuchokera kumwamba ndi kunditenga,+Anandivuula m’madzi akuya.+