Salimo 18:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Iye adzachititsa mapazi anga kukhala aliwiro ngati a mbawala zazikazi,+Ndipo adzandiimiritsabe pamalo okwezeka kwa ine.+ Habakuku 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ndiye mphamvu yanga.+ Iye adzachititsa miyendo yanga kukhala ngati ya mbawala,+ moti adzandiyendetsa pamalo anga okwezeka.”+Kwa wotsogolera nyimbo zoimbidwa ndi zipangizo zanga za zingwe.
33 Iye adzachititsa mapazi anga kukhala aliwiro ngati a mbawala zazikazi,+Ndipo adzandiimiritsabe pamalo okwezeka kwa ine.+
19 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ndiye mphamvu yanga.+ Iye adzachititsa miyendo yanga kukhala ngati ya mbawala,+ moti adzandiyendetsa pamalo anga okwezeka.”+Kwa wotsogolera nyimbo zoimbidwa ndi zipangizo zanga za zingwe.