Salimo 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yehova ndiye kuwala+ kwanga ndi chipulumutso changa.+Ndingaopenso ndani?+Yehova ndiye malo a chitetezo cha moyo wanga.+Ndingachitenso mantha ndi ndani?+ Aefeso 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kutinso mogwirizana ndi chuma+ cha ulemerero wake, akuloleni kuti munthu wanu wamkati+ akhale wamphamvu, mwa mphamvu ya mzimu wake,+ Afilipi 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pa zinthu zonse, ndimapeza mphamvu kuchokera kwa iye amene amandipatsa mphamvu.+ Akolose 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tikupemphereranso kuti mulandire mphamvu zazikulu chifukwa cha mphamvu zake zaulemerero,+ kuti muthe kupirira+ zinthu zonse ndi kukhala oleza mtima ndiponso achimwemwe,
27 Yehova ndiye kuwala+ kwanga ndi chipulumutso changa.+Ndingaopenso ndani?+Yehova ndiye malo a chitetezo cha moyo wanga.+Ndingachitenso mantha ndi ndani?+
16 Kutinso mogwirizana ndi chuma+ cha ulemerero wake, akuloleni kuti munthu wanu wamkati+ akhale wamphamvu, mwa mphamvu ya mzimu wake,+
11 Tikupemphereranso kuti mulandire mphamvu zazikulu chifukwa cha mphamvu zake zaulemerero,+ kuti muthe kupirira+ zinthu zonse ndi kukhala oleza mtima ndiponso achimwemwe,