Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 3:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Ndiyeno Davide anauza Yowabu ndi anthu onse amene anali pamenepo kuti: “Ng’ambani zovala zanu+ ndipo muvale ziguduli*+ kuti mulire maliro a Abineri.” Ngakhale Mfumu Davide nayenso anayenda pambuyo pa chithatha cha Abineri.

  • 2 Samueli 13:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Mfumu itamva zimenezi inaimirira ndi kung’amba zovala zake+ n’kugona pansi.+ Atumiki ake onse anaimirira pafupi ndi mfumuyo atang’ambanso zovala zawo.+

  • 2 Mbiri 34:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 chifukwa chakuti mtima wako+ unali wofewa ndipo unadzichepetsa+ chifukwa cha Mulungu utamva mawu ake okhudza malo ano ndi anthu ake, ndipo unadzichepetsa pamaso panga+ n’kung’amba+ zovala zako ndi kulira pamaso panga, ineyo ndamva,+ ndiwo mawu a Yehova.

  • Machitidwe 14:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma atumwiwo, Baranaba ndi Paulo, atamva zimenezi anang’amba malaya awo akunja ndi kuthamanga kukalowa m’khamu la anthu lija akufuula

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena