2 Samueli 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zitatero, Davide anatuma nthumwi kukafufuza za mkaziyo.+ Ndiyeno munthu wina ananena kuti: “Kodi ameneyu si Bati-seba+ mwana wa Eliyamu,*+ mkazi wa Uriya+ Mhiti?”+ Miyambo 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Imwa madzi ochokera m’chitsime chako, komanso madzi oyenderera kuchokera pakati pa chitsime chako.+
3 Zitatero, Davide anatuma nthumwi kukafufuza za mkaziyo.+ Ndiyeno munthu wina ananena kuti: “Kodi ameneyu si Bati-seba+ mwana wa Eliyamu,*+ mkazi wa Uriya+ Mhiti?”+
15 Imwa madzi ochokera m’chitsime chako, komanso madzi oyenderera kuchokera pakati pa chitsime chako.+