Mlaliki 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nthawi zonse zovala zako zizikhala zoyera,+ ndipo pamutu pako pasamasowe mafuta.+ Danieli 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Sindinadye chakudya chokoma, sindinadye nyama kapena kumwa vinyo ndipo sindinadzole mafuta kufikira milungu itatu yonseyo itatha.+
3 Sindinadye chakudya chokoma, sindinadye nyama kapena kumwa vinyo ndipo sindinadzole mafuta kufikira milungu itatu yonseyo itatha.+