Numeri 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi dzina la bambo athu lichotsedwe ku banja lawo chifukwa chakuti analibe mwana wamwamuna?+ Chonde, tipatseni cholowa pakati pa abale awo a bambo athu.”+ Deuteronomo 25:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwana woyamba amene mkaziyo angabereke, atenge dzina la mwamuna womwalira uja,+ kuti dzina la m’bale wake lisafafanizike mu Isiraeli.+
4 Kodi dzina la bambo athu lichotsedwe ku banja lawo chifukwa chakuti analibe mwana wamwamuna?+ Chonde, tipatseni cholowa pakati pa abale awo a bambo athu.”+
6 Mwana woyamba amene mkaziyo angabereke, atenge dzina la mwamuna womwalira uja,+ kuti dzina la m’bale wake lisafafanizike mu Isiraeli.+