Genesis 38:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma Onani anadziwa kuti anawo sadzakhala ake.+ Choncho, nthawi zonse akagona ndi mkazi wa m’bale wakeyo, anali kutaya pansi umuna wake kuti asam’berekere ana m’bale wakeyo.+ Rute 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Komanso ndikugula Rute Mmowabu, mkazi wa Maloni, kukhala mkazi wanga kuti dzina la mwamuna wake amene anamwalira+ libwerere pacholowa chake, kutinso lisafafanizike pakati pa abale ake ndi mumzinda wathu. Inu ndinu mboni+ lero.” Rute 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Zitatero akazi anayamba kuuza+ Naomi kuti: “Adalitsike Yehova,+ amene wachititsa kuti usasowe wokuwombola lero, kuti dzina lake lifalitsidwe mu Isiraeli.
9 Koma Onani anadziwa kuti anawo sadzakhala ake.+ Choncho, nthawi zonse akagona ndi mkazi wa m’bale wakeyo, anali kutaya pansi umuna wake kuti asam’berekere ana m’bale wakeyo.+
10 Komanso ndikugula Rute Mmowabu, mkazi wa Maloni, kukhala mkazi wanga kuti dzina la mwamuna wake amene anamwalira+ libwerere pacholowa chake, kutinso lisafafanizike pakati pa abale ake ndi mumzinda wathu. Inu ndinu mboni+ lero.”
14 Zitatero akazi anayamba kuuza+ Naomi kuti: “Adalitsike Yehova,+ amene wachititsa kuti usasowe wokuwombola lero, kuti dzina lake lifalitsidwe mu Isiraeli.