1 Samueli 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno Eli anamuuza kuti: “Kodi Mulungu wakuuza chiyani? Chonde usandibisire ayi.+ Mulungu akulange ndi kuwonjezerapo,+ ukandibisira ngakhale mawu amodzi pa mawu onse amene iye wakuuza.” Aefeso 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Chotero, popeza tsopano mwataya chinyengo,+ aliyense wa inu alankhule zoona kwa mnzake,+ chifukwa ndife ziwalo za thupi limodzi.+
17 Ndiyeno Eli anamuuza kuti: “Kodi Mulungu wakuuza chiyani? Chonde usandibisire ayi.+ Mulungu akulange ndi kuwonjezerapo,+ ukandibisira ngakhale mawu amodzi pa mawu onse amene iye wakuuza.”
25 Chotero, popeza tsopano mwataya chinyengo,+ aliyense wa inu alankhule zoona kwa mnzake,+ chifukwa ndife ziwalo za thupi limodzi.+