Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 12:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndiyeno Yehova wanena kuti, ‘Taona, ndikukugwetsera tsoka m’nyumba yako yomwe.+ Ndidzatenga akazi ako iwe ukuona ndi kuwapereka kwa mwamuna wina,+ ndipo iye adzagona ndi akazi ako anthu onse akuona.+

  • 2 Samueli 15:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Nthawi yomweyo, Davide anauza atumiki ake onse amene anali naye limodzi mu Yerusalemu, kuti: “Nyamukani, tiyeni tithawe,+ pakuti sipapezeka munthu wopulumuka m’manja mwa Abisalomu. Chitani changu, pakuti mwina angafike mofulumira ndi kutipeza n’kutichitira choipa komanso kukantha mzinda ndi lupanga!”+

  • 2 Samueli 17:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ukatero, tikamuukire kumene tikudziwa kuti tikhoza kum’peza,+ ndipo tikam’fikira ngati mmene mame+ amagwera pansi. Pamenepo sipadzakhala aliyense wopulumuka, iyeyo ngakhale amuna onse amene ali naye.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena