1 Samueli 23:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mukaonetsetse ndi kutsimikizira za malo onse obisika kumene iye amabisala. Kenako mudzabwerenso kwa ine ndi umboni, ndipo ine ndidzapita nanu. Ngati alidi m’dzikolo, ndidzam’funafuna mosamala pakati pa anthu masauzande+ ambirimbiriwo a Yuda.” 2 Samueli 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipotu panopa akubisala+ m’dzenje linalake kapena m’malo ena. Ndiyeno iyeyo akakhala woyamba kuukira anthu, nkhani idzafala kuti, ‘Anthu amene akutsatira Abisalomu agonjetsedwa!’
23 Mukaonetsetse ndi kutsimikizira za malo onse obisika kumene iye amabisala. Kenako mudzabwerenso kwa ine ndi umboni, ndipo ine ndidzapita nanu. Ngati alidi m’dzikolo, ndidzam’funafuna mosamala pakati pa anthu masauzande+ ambirimbiriwo a Yuda.”
9 Ndipotu panopa akubisala+ m’dzenje linalake kapena m’malo ena. Ndiyeno iyeyo akakhala woyamba kuukira anthu, nkhani idzafala kuti, ‘Anthu amene akutsatira Abisalomu agonjetsedwa!’